Zofunika mu galamala wa Chichewa

Zofunika mu Galamala wa Chichewa ndi buku lomwe lakonzedwanso molingana ndi ndondomeko ya maphunziro yatsopano yomwe a za unduna wa maphunziro anakonzanso mu chaka cha 2013.

MK21,500.00

ISBN. 978 99908 17 006 Category:

About The Author

I.J.A Nankwenya

Zofunika mu Galamala wa Chichewa ndi buku lomwe lakonzedwanso molingana ndi ndondomeko ya maphunziro yatsopano yomwe a za unduna wa maphunziro anakonzanso mu chaka cha 2013.

Mu bukuli, mwaonjezeredwa ntchito zoti ophunzira achite pofuna kumvetsetsa za zomwe aphunzira. Njira yotere idzathandiza mphunzitsi kuona mosavuta ngati Ophunzira amvetsetsa ndipo aphunzira kathu.

Buku lokonzedwansoli lithandiza ophunzira kumvetsetsa za chiyankhulo ndi kukonzekera mayeso awo pa mapeto a maphunziro a sekondale.

Buku la Zofunika mu Galamala wa Chichewa ndi buku labwino ndi lothandiza ophunzira komanso mphunzitsi wa chiyankhulo cha Chichewa.

Reviews

There are no reviews yet.

Be the first to review “Zofunika mu galamala wa Chichewa”

Your email address will not be published. Required fields are marked *